Salimo 49:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzatchera khutu kuti ndimvetsere mwambi.+Poimba zeze ndidzamasulira mawu anga ophiphiritsa.+ Salimo 78:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzatsegula pakamwa panga ndi kunena mwambi.+Ndidzanena mawu ophiphiritsa akalekale,+