1 Mafumu 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zombo+ za Hiramu zimene zinabweretsa golide kuchokera ku Ofiri,+ zinabweretsanso matabwa a mtengo wa m’bawa+ ochuluka zedi ndi miyala yamtengo wapatali.+ 1 Mbiri 29:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chumacho chili motere: Matalente* 3,000 a golide wa ku Ofiri,+ matalente 7,000 a siliva woyengedwa bwino wokutira makoma a nyumbazo, Salimo 45:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ana aakazi+ a mafumu ali m’gulu la akazi ako okondedwa.Mkazi wamkulu wa mfumu+ waima kudzanja lako lamanja atavala zovala zagolide wa ku Ofiri.+
11 Zombo+ za Hiramu zimene zinabweretsa golide kuchokera ku Ofiri,+ zinabweretsanso matabwa a mtengo wa m’bawa+ ochuluka zedi ndi miyala yamtengo wapatali.+
4 Chumacho chili motere: Matalente* 3,000 a golide wa ku Ofiri,+ matalente 7,000 a siliva woyengedwa bwino wokutira makoma a nyumbazo,
9 Ana aakazi+ a mafumu ali m’gulu la akazi ako okondedwa.Mkazi wamkulu wa mfumu+ waima kudzanja lako lamanja atavala zovala zagolide wa ku Ofiri.+