Miyambo 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti nzeru n’zamtengo wapatali kuposa miyala ya korali,+ ndipo zosangalatsa zonse sizingafanane nazo.+ Miyambo 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pali golide komanso miyala yamtengo wapatali ya korali yambirimbiri, koma milomo yodziwa zinthu ndiyo ziwiya zamtengo wapatali.+
11 Pakuti nzeru n’zamtengo wapatali kuposa miyala ya korali,+ ndipo zosangalatsa zonse sizingafanane nazo.+
15 Pali golide komanso miyala yamtengo wapatali ya korali yambirimbiri, koma milomo yodziwa zinthu ndiyo ziwiya zamtengo wapatali.+