Miyambo 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 N’zamtengo wapatali kuposa miyala ya korali,+ ndipo zonse zimene umakonda sizingafanane nazo. Miyambo 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Landirani malangizo* anga osati siliva, ndiponso kudziwa zinthu m’malo mwa golide wabwino kwambiri.+ Mlaliki 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuwonjezera pa kukhala ndi nzeru,+ wosonkhanitsayo nthawi zonse anali kuphunzitsanso anthuwo kuti adziwe zinthu.+ Anali kusinkhasinkha ndi kufufuza zinthu mosamala,+ ndipo analemba miyambi yambiri m’ndondomeko yoyenera.+ Aefeso 4:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mawu alionse owola asatuluke pakamwa panu,+ koma alionse olimbikitsa monga mmene kungafunikire, kuti asangalatse owamva.+
10 Landirani malangizo* anga osati siliva, ndiponso kudziwa zinthu m’malo mwa golide wabwino kwambiri.+
9 Kuwonjezera pa kukhala ndi nzeru,+ wosonkhanitsayo nthawi zonse anali kuphunzitsanso anthuwo kuti adziwe zinthu.+ Anali kusinkhasinkha ndi kufufuza zinthu mosamala,+ ndipo analemba miyambi yambiri m’ndondomeko yoyenera.+
29 Mawu alionse owola asatuluke pakamwa panu,+ koma alionse olimbikitsa monga mmene kungafunikire, kuti asangalatse owamva.+