Salimo 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pakuti inu Yehova mudzandiyatsira nyale yanga,+Mulungu wanga adzandiunikira mu mdima.+ Salimo 119:105 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 105 Mawu anu ndi nyale younikira kumapazi anga,+Ndi kuwala kounikira njira yanga.+