Salimo 78:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Koma iwo anali kufuna kum’pusitsa ndi pakamwa pawo.+Ndi lilime lawo anali kufuna kunena bodza kwa iye.+ 2 Akorinto 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Aka ndi kachitatu+ tsopano kukonza ulendo wobwera kwanuko. “Muzitsimikizira nkhani iliyonse mutamva umboni wa pakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu.”+ Tito 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 N’kofunika kuwatseka pakamwa, pakuti anthu amenewa, pofuna kupeza phindu mwachinyengo,+ akuwonongabe mabanja athunthu+ mwa kuphunzitsa zinthu zimene sayenera kuphunzitsa.
36 Koma iwo anali kufuna kum’pusitsa ndi pakamwa pawo.+Ndi lilime lawo anali kufuna kunena bodza kwa iye.+
13 Aka ndi kachitatu+ tsopano kukonza ulendo wobwera kwanuko. “Muzitsimikizira nkhani iliyonse mutamva umboni wa pakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu.”+
11 N’kofunika kuwatseka pakamwa, pakuti anthu amenewa, pofuna kupeza phindu mwachinyengo,+ akuwonongabe mabanja athunthu+ mwa kuphunzitsa zinthu zimene sayenera kuphunzitsa.