Salimo 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti ndinu amene munanditulutsa m’mimba,+Amene munandichititsa kumva kuti ndine wotetezeka pamene ndinali kuyamwa mabere a mayi anga.+ Luka 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chifukwa masiku akubwera pamene anthu adzanena kuti, ‘Odala ndi akazi osabereka, amene sanaberekepo, komanso amene mabere awo sanayamwitsepo!’+
9 Pakuti ndinu amene munanditulutsa m’mimba,+Amene munandichititsa kumva kuti ndine wotetezeka pamene ndinali kuyamwa mabere a mayi anga.+
29 Chifukwa masiku akubwera pamene anthu adzanena kuti, ‘Odala ndi akazi osabereka, amene sanaberekepo, komanso amene mabere awo sanayamwitsepo!’+