Yobu 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chonsecho mukudziwa kuti ndine wosalakwa,+Ndipo palibe wondipulumutsa m’manja mwanu.+ Yobu 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chonsecho manja anga sanachite zachiwawa,Ndipo pemphero langa ndi loyera.+ Yobu 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mapazi anga amatsata mayendedwe ake.Ndasunga njira yake, ndipo sindipatukapo.+