Yobu 29:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndinkavala chilungamo, ndipo icho chinkandiveka.+Chilungamo changa chinali ngati malaya akunja odula manja, ndi nduwira.* Miyambo 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Njira iliyonse ya munthu imaoneka yowongoka m’maganizo mwake,+ koma Yehova amafufuza mitima.+
14 Ndinkavala chilungamo, ndipo icho chinkandiveka.+Chilungamo changa chinali ngati malaya akunja odula manja, ndi nduwira.*