Deuteronomo 34:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mose anamwalira ali ndi zaka 120.+ Diso lake silinachite mdima+ ndipo anali adakali ndi mphamvu.+ Yobu 42:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pambuyo pa zimenezi, Yobu anakhala ndi moyo zaka 140+ ndipo anaona ana ake ndi zidzukulu zake+ mpaka m’badwo wachinayi. Salimo 103:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Amene akukukhutiritsa pa nthawi ya moyo wako ndi zinthu zabwino.+Mulungu akukuchititsa kukhalabe wachinyamata ndi wamphamvu ngati chiwombankhanga.+
16 Pambuyo pa zimenezi, Yobu anakhala ndi moyo zaka 140+ ndipo anaona ana ake ndi zidzukulu zake+ mpaka m’badwo wachinayi.
5 Amene akukukhutiritsa pa nthawi ya moyo wako ndi zinthu zabwino.+Mulungu akukuchititsa kukhalabe wachinyamata ndi wamphamvu ngati chiwombankhanga.+