Yesaya 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mukakhala ndi mtima wofuna kundimvera, mudzadya zabwino za m’dziko lanu.+ Yeremiya 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano konzani njira zanu ndi zochita zanu kuti zikhale zabwino+ ndipo muzimvera mawu a Yehova Mulungu wanu. Mukatero, Yehova adzasintha maganizo ake pa tsoka limene wanena kuti akugwetserani.+
13 Tsopano konzani njira zanu ndi zochita zanu kuti zikhale zabwino+ ndipo muzimvera mawu a Yehova Mulungu wanu. Mukatero, Yehova adzasintha maganizo ake pa tsoka limene wanena kuti akugwetserani.+