Salimo 103:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Sanatichitire mogwirizana ndi machimo athu,+Kapena kutipatsa chilango chogwirizana ndi zolakwa zathu.+ Yeremiya 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 ndiyeno anthuwo n’kusiya zoipa zimene anali kuchita, zimene ndinawadzudzula nazo,+ pamenepo ndidzasintha maganizo anga kuti ndisawagwetsere tsoka limene ndinafuna kuwagwetsera.+ Yeremiya 36:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwina anthu a m’nyumba ya Yuda adzamva za masoka onse amene ndikufuna kuwagwetsera+ ndipo aliyense abwerera ndi kusiya njira yake yoipa.+ Akatero, ine ndidzawakhululukira zolakwa zawo ndi machimo awo.”+ Ezekieli 18:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “‘Inetu sindisangalala ndi imfa ya munthu aliyense,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. ‘Choncho tembenukani anthu inu, kuti mukhale ndi moyo.’”+ Yona 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndani angadziwe? Mwina Mulungu woona satigwetsera tsoka ndipo asintha maganizo+ ndi kubweza mkwiyo wake woyaka moto, moti satiwononga.”+
10 Sanatichitire mogwirizana ndi machimo athu,+Kapena kutipatsa chilango chogwirizana ndi zolakwa zathu.+
8 ndiyeno anthuwo n’kusiya zoipa zimene anali kuchita, zimene ndinawadzudzula nazo,+ pamenepo ndidzasintha maganizo anga kuti ndisawagwetsere tsoka limene ndinafuna kuwagwetsera.+
3 Mwina anthu a m’nyumba ya Yuda adzamva za masoka onse amene ndikufuna kuwagwetsera+ ndipo aliyense abwerera ndi kusiya njira yake yoipa.+ Akatero, ine ndidzawakhululukira zolakwa zawo ndi machimo awo.”+
32 “‘Inetu sindisangalala ndi imfa ya munthu aliyense,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. ‘Choncho tembenukani anthu inu, kuti mukhale ndi moyo.’”+
9 Ndani angadziwe? Mwina Mulungu woona satigwetsera tsoka ndipo asintha maganizo+ ndi kubweza mkwiyo wake woyaka moto, moti satiwononga.”+