Salimo 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ananditenga ndi kundiika pamalo otakasuka.+Anandipulumutsa chifukwa anakondwera nane.+ Salimo 31:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Simunandipereke m’manja mwa adani.+Mwapondetsa phazi langa pamalo otakasuka.+ Salimo 118:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 M’masautso anga ndinaitana Ya.+Ya anandiyankha ndi kundiika pamalo otakasuka.+