Yesaya 40:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kodi anafunsirapo nzeru kwa ndani kuti amuthandize kumvetsetsa zinthu? Ndani amamuphunzitsa njira ya chilungamo? Ndani amamuphunzitsa kuti azidziwa zinthu,+ ndipo ndani amamuphunzitsa kuti akhale womvetsa bwino zinthu?+
14 Kodi anafunsirapo nzeru kwa ndani kuti amuthandize kumvetsetsa zinthu? Ndani amamuphunzitsa njira ya chilungamo? Ndani amamuphunzitsa kuti azidziwa zinthu,+ ndipo ndani amamuphunzitsa kuti akhale womvetsa bwino zinthu?+