Salimo 37:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pa nthawi yatsoka sadzachita manyazi,+Ndipo pa nthawi ya njala adzakhuta.+