Salimo 40:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Onse amene akufunafuna moyo wanga kuti aufafanize+Achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+Amene akukondwera ndi tsoka langa abwerere ndipo anyazitsidwe.+ Salimo 70:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amene akufunafuna moyo wanga achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+Amene akukondwera ndi tsoka langa abwerere ndipo anyazitsidwe.+ Yeremiya 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthu amene amandizunza achite manyazi+ koma musalole kuti ineyo ndichite manyazi.+ Anthuwo agwidwe ndi mantha aakulu koma musalole kuti ine ndigwidwe ndi mantha aakulu. Agwetsereni tsoka+ ndipo muwaphwanye kuwirikiza kawiri.+
14 Onse amene akufunafuna moyo wanga kuti aufafanize+Achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+Amene akukondwera ndi tsoka langa abwerere ndipo anyazitsidwe.+
2 Amene akufunafuna moyo wanga achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+Amene akukondwera ndi tsoka langa abwerere ndipo anyazitsidwe.+
18 Anthu amene amandizunza achite manyazi+ koma musalole kuti ineyo ndichite manyazi.+ Anthuwo agwidwe ndi mantha aakulu koma musalole kuti ine ndigwidwe ndi mantha aakulu. Agwetsereni tsoka+ ndipo muwaphwanye kuwirikiza kawiri.+