Yeremiya 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma inu Yehova mukudziwa bwino chiwembu chimene andikonzera kuti andiphe.+ Musakhululukire* cholakwa chawo, ndipo musafafanize tchimo lawolo pamaso panu. Koma iwo apunthwe pamaso panu.+ Muwachitire zimenezi pa nthawi ya mkwiyo wanu.+
23 Koma inu Yehova mukudziwa bwino chiwembu chimene andikonzera kuti andiphe.+ Musakhululukire* cholakwa chawo, ndipo musafafanize tchimo lawolo pamaso panu. Koma iwo apunthwe pamaso panu.+ Muwachitire zimenezi pa nthawi ya mkwiyo wanu.+