Miyambo 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Wosafulumira kukwiya n’ngozindikira zinthu kwambiri,+ koma wokwiya msanga amalimbikitsa uchitsiru.+ Miyambo 16:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Munthu wosakwiya msanga ndi wabwino kuposa munthu wamphamvu,+ ndipo munthu wolamulira mtima wake amaposa munthu wogonjetsa mzinda.+ Aefeso 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kwiyani, koma musachimwe.+ Dzuwa lisalowe muli chikwiyire,+
29 Wosafulumira kukwiya n’ngozindikira zinthu kwambiri,+ koma wokwiya msanga amalimbikitsa uchitsiru.+
32 Munthu wosakwiya msanga ndi wabwino kuposa munthu wamphamvu,+ ndipo munthu wolamulira mtima wake amaposa munthu wogonjetsa mzinda.+