Salimo 92:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti taonani adani anu, inu Yehova!+Adani anu onse adzatha!+Anthu onse ochita zopweteka anzawo adzamwazikana.+ Miyambo 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu akamakumbukira zabwino zimene munthu wolungama anali kuchita, amam’dalitsa,+ koma dzina la anthu oipa lidzawola.+ 2 Petulo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipo anthu amenewa, mofanana ndi nyama zopanda nzeru zimene zimabadwira kuti zidzagwidwe ndi kuwonongedwa, amalankhula monyoza za zinthu zimene sakuzidziwa,+ moti adzawonongedwa chifukwa cha njira yawo yachiwonongeko,
9 Pakuti taonani adani anu, inu Yehova!+Adani anu onse adzatha!+Anthu onse ochita zopweteka anzawo adzamwazikana.+
7 Anthu akamakumbukira zabwino zimene munthu wolungama anali kuchita, amam’dalitsa,+ koma dzina la anthu oipa lidzawola.+
12 Ndipo anthu amenewa, mofanana ndi nyama zopanda nzeru zimene zimabadwira kuti zidzagwidwe ndi kuwonongedwa, amalankhula monyoza za zinthu zimene sakuzidziwa,+ moti adzawonongedwa chifukwa cha njira yawo yachiwonongeko,