Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 24:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “Ukaiwala mtolo wa tirigu pokolola m’munda wako,+ usabwerere kukatenga mtolowo. Uzisiyira mlendo wokhala m’dziko lanu, mwana wamasiye ndi mkazi wamasiye.+ Uzichita zimenezi kuti Yehova Mulungu wako akudalitse pa chilichonse chimene dzanja lako likuchita.+

  • Salimo 25:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Moyo wake udzasangalala ndi ubwino wa Mulungu,+

      Mbadwa zake zidzatenga dziko lapansi kukhala lawo.+

  • Salimo 112:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Ana ake adzakhala amphamvu padziko lapansi.+

      ד [Daʹleth]

      Ndipo m’badwo wa anthu olungama udzadalitsidwa.+

  • Salimo 145:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Zolengedwa zonse zimayang’ana kwa inu mwachiyembekezo,+

      Ndipo mumazipatsa chakudya pa nyengo yake.+

  • Miyambo 10:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Yehova sadzachititsa munthu wolungama kukhala ndi njala,+ koma zolakalaka za anthu oipa adzazikankhira kumbali.+

  • Miyambo 13:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Munthu wabwino adzasiyira cholowa zidzukulu zake, ndipo chuma cha wochimwa chimasungidwa kuti chidzakhale cha munthu wolungama.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena