Salimo 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndidzalengeza dzina lanu+ kwa abale anga.+Ndidzakutamandani pakati pa mpingo.+ Salimo 35:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndidzakutamandani mu mpingo waukulu.+Ndidzakutamandani pakati pa anthu ambiri.+