Salimo 110:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu ako+ adzadzipereka mofunitsitsa+ pa tsiku limene udzatsogolera asilikali ako kunkhondo.+Wadzikongoletsa ndi ulemerero,+Ndipo gulu la achinyamata amene ali ngati mame a m’bandakucha lili pamodzi ndi iwe.+ Mateyu 26:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Khalani maso+ ndipo pempherani+ kosalekeza kuti musalowe m’mayesero.+ Zoona, mzimu ndi wofunitsitsa, koma thupi ndi lofooka.”+
3 Anthu ako+ adzadzipereka mofunitsitsa+ pa tsiku limene udzatsogolera asilikali ako kunkhondo.+Wadzikongoletsa ndi ulemerero,+Ndipo gulu la achinyamata amene ali ngati mame a m’bandakucha lili pamodzi ndi iwe.+
41 Khalani maso+ ndipo pempherani+ kosalekeza kuti musalowe m’mayesero.+ Zoona, mzimu ndi wofunitsitsa, koma thupi ndi lofooka.”+