Salimo 28:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti iwo salabadira zochita za Yehova,+Kapena ntchito za manja ake.+Mulungu sadzawamanga koma adzawapasula. Salimo 37:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti ochita zoipa adzaphedwa.+Koma oyembekezera Yehova ndi amene adzalandire dziko lapansi.+
5 Pakuti iwo salabadira zochita za Yehova,+Kapena ntchito za manja ake.+Mulungu sadzawamanga koma adzawapasula.