Numeri 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Komanso, pali ine Mulungu wamoyo, dziko lonse lapansi lidzadzaza ndi ulemerero wa Yehova.+ Salimo 72:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Lidalitsike dzina lake laulemerero mpaka kalekale,+Ndipo ulemerero wake udzaze dziko lonse lapansi.+Ame! Ame!*
19 Lidalitsike dzina lake laulemerero mpaka kalekale,+Ndipo ulemerero wake udzaze dziko lonse lapansi.+Ame! Ame!*