Salimo 43:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzapita paguwa lansembe la Mulungu,+Kwa Mulungu amene amandikondweretsa ndi kundisangalatsa.+Ndipo ndidzakutamandani ndi zeze, inu Mulungu, Mulungu wanga.+ Salimo 71:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndikafuna kuimba nyimbo zokutamandani, pakamwa panga padzafuula mokondwera,+Ngakhalenso moyo wanga umene mwauwombola+ udzakutamandani. Salimo 135:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tamandani Ya, pakuti Yehova ndi wabwino.+Muimbireni nyimbo zotamanda dzina lake, pakuti kuchita zimenezi n’kosangalatsa.+
4 Ndidzapita paguwa lansembe la Mulungu,+Kwa Mulungu amene amandikondweretsa ndi kundisangalatsa.+Ndipo ndidzakutamandani ndi zeze, inu Mulungu, Mulungu wanga.+
23 Ndikafuna kuimba nyimbo zokutamandani, pakamwa panga padzafuula mokondwera,+Ngakhalenso moyo wanga umene mwauwombola+ udzakutamandani.
3 Tamandani Ya, pakuti Yehova ndi wabwino.+Muimbireni nyimbo zotamanda dzina lake, pakuti kuchita zimenezi n’kosangalatsa.+