Salimo 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti m’kamwa mwawo simutuluka mawu okhulupirika.+Mitima yawo yadzaza ndi zinthu zoipa.+Mmero wawo ndi manda otseguka.+Iwo amalankhula ndi lilime lachinyengo.+ Yeremiya 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Mtima ndi wonyenga kwambiri kuposa china chilichonse ndipo ungathe kuchita china chilichonse choipa.*+ Ndani angaudziwe?
9 Pakuti m’kamwa mwawo simutuluka mawu okhulupirika.+Mitima yawo yadzaza ndi zinthu zoipa.+Mmero wawo ndi manda otseguka.+Iwo amalankhula ndi lilime lachinyengo.+
9 “Mtima ndi wonyenga kwambiri kuposa china chilichonse ndipo ungathe kuchita china chilichonse choipa.*+ Ndani angaudziwe?