Deuteronomo 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye ndi amene muyenera kum’tamanda,+ ndipo iye ndi Mulungu wanu amene wakuchitirani zinthu zazikulu ndi zochititsa mantha, zimene mwaziona ndi maso anu.+ Salimo 47:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti Yehova, Wam’mwambamwamba, ndi wochititsa mantha,+Ndiye Mfumu yaikulu padziko lonse lapansi.+ Chivumbulutso 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo akuimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu, ndi nyimbo ya Mwanawankhosa,+ yakuti: “Ntchito zanu n’zazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama ndi zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+
21 Iye ndi amene muyenera kum’tamanda,+ ndipo iye ndi Mulungu wanu amene wakuchitirani zinthu zazikulu ndi zochititsa mantha, zimene mwaziona ndi maso anu.+
2 Pakuti Yehova, Wam’mwambamwamba, ndi wochititsa mantha,+Ndiye Mfumu yaikulu padziko lonse lapansi.+
3 Iwo akuimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu, ndi nyimbo ya Mwanawankhosa,+ yakuti: “Ntchito zanu n’zazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama ndi zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+