Genesis 27:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mulungu woona akupatse mame akumwamba,+ ndi nthaka yachonde ya dziko lapansi.+ Achulukitsenso zokolola zako ndi vinyo wako watsopano.+ Deuteronomo 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Lidalitsidwe ndi zinthu zabwino kwambiri za padziko lapansi, ndi chuma chake chonse,+Komanso movomerezedwa ndi Iye amene anaonekera m’chitsamba chaminga.+Zimenezi zikhale pamutu pa Yosefe,+Paliwombo pa munthu wopatulidwa pakati pa abale ake.+
28 Mulungu woona akupatse mame akumwamba,+ ndi nthaka yachonde ya dziko lapansi.+ Achulukitsenso zokolola zako ndi vinyo wako watsopano.+
16 Lidalitsidwe ndi zinthu zabwino kwambiri za padziko lapansi, ndi chuma chake chonse,+Komanso movomerezedwa ndi Iye amene anaonekera m’chitsamba chaminga.+Zimenezi zikhale pamutu pa Yosefe,+Paliwombo pa munthu wopatulidwa pakati pa abale ake.+