Deuteronomo 32:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Kondwerani, mitundu inu, pamodzi ndi anthu ake,+Pakuti adzabwezera magazi a atumiki ake,+Ndipo adzabwezera chilango kwa adani ake,+Nadzaphimba machimo a dziko la anthu ake.” Aroma 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Komanso Malemba amati: “Kondwerani, mitundu inu, pamodzi ndi anthu ake.”+
43 Kondwerani, mitundu inu, pamodzi ndi anthu ake,+Pakuti adzabwezera magazi a atumiki ake,+Ndipo adzabwezera chilango kwa adani ake,+Nadzaphimba machimo a dziko la anthu ake.”