Numeri 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova akukomereni mtima,+ ndipo akuyanjeni.+ Salimo 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pali ambiri amene akunena kuti: “Ndani adzationetsa zinthu zabwino?”Inu Yehova, tiunikeni ndi kuwala kwa nkhope yanu.+ Salimo 31:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndikomereni mtima ine mtumiki wanu.+Ndipulumutseni mwa kukoma mtima kwanu kosatha.+ Salimo 119:135 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 135 Ndikomereni mtima ine mtumiki wanu,+Ndipo ndiphunzitseni malamulo anu.+ Miyambo 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Nkhope ya mfumu ikawala, zimatanthauza moyo.+ Ndipo mafuno ake abwino ali ngati mtambo wa mvula yomalizira.+
6 Pali ambiri amene akunena kuti: “Ndani adzationetsa zinthu zabwino?”Inu Yehova, tiunikeni ndi kuwala kwa nkhope yanu.+
15 Nkhope ya mfumu ikawala, zimatanthauza moyo.+ Ndipo mafuno ake abwino ali ngati mtambo wa mvula yomalizira.+