Salimo 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndalefuka chifukwa cha kuusa moyo* kwanga.+Usiku wonse ndimanyowetsa bedi langa.+Ndimakhathamitsa bedi langa ndi misozi.+ Salimo 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Mulungu wanga, ine ndimaitana usana koma simundiyankha.+Usiku ndimaitanabe, moti sindikukhala chete.+
6 Ndalefuka chifukwa cha kuusa moyo* kwanga.+Usiku wonse ndimanyowetsa bedi langa.+Ndimakhathamitsa bedi langa ndi misozi.+
2 Inu Mulungu wanga, ine ndimaitana usana koma simundiyankha.+Usiku ndimaitanabe, moti sindikukhala chete.+