Salimo 89:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Dzanja langa lolimba lidzakhala pa iye.+Mkono wanga udzamulimbitsa.+ Salimo 110:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 110 Yehova wauza Ambuye wanga kuti:+“Khala kudzanja langa lamanja+Kufikira nditaika adani ako monga chopondapo mapazi ako.”+
110 Yehova wauza Ambuye wanga kuti:+“Khala kudzanja langa lamanja+Kufikira nditaika adani ako monga chopondapo mapazi ako.”+