-
Salimo 2:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Mafumu a dziko lapansi aima pamalo awo,+
Ndipo nduna zapamwamba zasonkhana pamodzi mogwirizana.+
Atero kuti alimbane ndi Yehova+ komanso wodzozedwa wake.+
-
Yesaya 7:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 popeza Siriya ndi Efuraimu ndiponso mwana wa Remaliya akukonzera zoipa ndipo anena kuti:
-
-
-