Yobu 33:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iye wandiwombola kuti ndisapite kudzenje,+Ndipo moyo wanga udzaona kuwala.’ Salimo 56:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti inu mwalanditsa moyo wanga ku imfa.+Inu mwateteza phazi langa kuti lisapunthwe,+Kuti ndiyendeyende pamaso pa Mulungu m’kuwala kumene kumaunikira anthu amoyo.+ Salimo 116:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti inu mwapulumutsa moyo wanga ku imfa,+Mwateteza maso anga kuti asakhetse misozi ndiponso phazi langa kuti lisapunthwe.+
13 Pakuti inu mwalanditsa moyo wanga ku imfa.+Inu mwateteza phazi langa kuti lisapunthwe,+Kuti ndiyendeyende pamaso pa Mulungu m’kuwala kumene kumaunikira anthu amoyo.+
8 Pakuti inu mwapulumutsa moyo wanga ku imfa,+Mwateteza maso anga kuti asakhetse misozi ndiponso phazi langa kuti lisapunthwe.+