Salimo 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mbewu idzamutumikira.+Adzalengeza za Yehova ku m’badwo wotsatira.+ Luka 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Komano, musakondwere ndi zimenezi, kuti mizimu yakugonjerani, koma kondwerani chifukwa mayina+ anu alembedwa kumwamba.”
20 Komano, musakondwere ndi zimenezi, kuti mizimu yakugonjerani, koma kondwerani chifukwa mayina+ anu alembedwa kumwamba.”