Salimo 87:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndidzatchula Rahabi*+ ndi Babulo+ monga ena mwa amene akundidziwa.Ponena za Filisitiya,+ Turo ndi Kusi ine ndidzati:“Amenewa anabadwira m’Ziyoni.”+ Agalatiya 4:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma monga mmene zinalili pa nthawiyo, kuti wobadwa monga mmene ana onse amabadwira anayamba kuzunza+ wobadwa mwa mzimu, ndi mmenenso zilili masiku ano.+
4 Ine ndidzatchula Rahabi*+ ndi Babulo+ monga ena mwa amene akundidziwa.Ponena za Filisitiya,+ Turo ndi Kusi ine ndidzati:“Amenewa anabadwira m’Ziyoni.”+
29 Koma monga mmene zinalili pa nthawiyo, kuti wobadwa monga mmene ana onse amabadwira anayamba kuzunza+ wobadwa mwa mzimu, ndi mmenenso zilili masiku ano.+