Agalatiya 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kunena za ine abale, ngati ndimalalikirabe kuti anthu azidulidwa, n’chifukwa chiyani ndikuzunzidwabe? Ndithudi, mtengo wozunzikirapo,+ womwe ndi chopunthwitsa,+ ukanakhala utachotsedwa.+ Agalatiya 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Onse ofuna kudzionetsa ngati abwino pamaso pa anthu ndi amene akukuumirizani kuti muzidulidwa.+ Akuchita zimenezi kuti asazunzidwe chifukwa cha mtengo wozunzikirapo wa Khristu,+ amene ndi Yesu.
11 Kunena za ine abale, ngati ndimalalikirabe kuti anthu azidulidwa, n’chifukwa chiyani ndikuzunzidwabe? Ndithudi, mtengo wozunzikirapo,+ womwe ndi chopunthwitsa,+ ukanakhala utachotsedwa.+
12 Onse ofuna kudzionetsa ngati abwino pamaso pa anthu ndi amene akukuumirizani kuti muzidulidwa.+ Akuchita zimenezi kuti asazunzidwe chifukwa cha mtengo wozunzikirapo wa Khristu,+ amene ndi Yesu.