Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 10:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Pa tsiku lanu losangalala,+ pa nyengo ya zikondwerero zanu,+ ndi pa masiku oyambira miyezi,+ muziliza malipengawo popereka nsembe zanu zopsereza+ ndi zachiyanjano.+ Kuliza malipengawo kudzakhala chikumbutso kwa Mulungu wanu. Ine ndine Yehova Mulungu wanu.”+

  • 1 Mbiri 15:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Aisiraeli onse anali kupita ndi likasa la pangano la Yehova akufuula mokondwera,+ ndiponso akuliza nyanga za nkhosa+ ndi malipenga.+ Iwo anali kuimbanso mokweza zinganga,+ zoimbira za zingwe, ndi azeze.+

  • 2 Mbiri 29:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Kenako Hezekiya anawauza kuti apereke nsembe yopsereza paguwa lansembe. Atayamba kupereka nsembe yopserezayo, nyimbo+ ya Yehova inayamba kuimbidwa limodzi ndi malipenga amene ankatsatira zipangizo zoimbira za Davide mfumu ya Isiraeli.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena