Ekisodo 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo Mose anatenga hafu ya magazi ndi kuwaika m’mbale zolowa,+ ndipo hafu inayo anawaza paguwa lansembe.+ Numeri 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chonde, khululukani kulakwa kwa anthuwa mwa kukoma mtima kwanu kosatha, ngati mmene mwakhala mukuwakhululukira kuchokera ku Iguputo mpaka pano.”+
6 Pamenepo Mose anatenga hafu ya magazi ndi kuwaika m’mbale zolowa,+ ndipo hafu inayo anawaza paguwa lansembe.+
19 Chonde, khululukani kulakwa kwa anthuwa mwa kukoma mtima kwanu kosatha, ngati mmene mwakhala mukuwakhululukira kuchokera ku Iguputo mpaka pano.”+