-
Nehemiya 9:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 “Inu ndinu Yehova, inu nokha.+ Ndinu amene munapanga kumwamba,+ ngakhale kumwambamwamba ndi makamu ake onse.+ Ndinu amene munapanga dziko lapansi+ ndi zonse zili momwemo+ komanso nyanja+ ndi zonse zili momwemo.+ Ndinu amene mukusunga zinthu zonse kuti zikhale ndi moyo. Ndipo makamu+ akumwamba amakugwadirani.
-
-
Salimo 136:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Yamikani woyala dziko lapansi pamwamba pa madzi:+
Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
-