Numeri 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Aroni, kuti: “Iwe udzakhala wopanda cholowa m’dziko mwawo, ndipo sudzapatsidwa gawo lililonse pakati pawo.+ Ine ndine gawo lako ndi cholowa chako pakati pa ana a Isiraeli.+ Salimo 73:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Thupi langa ndi mtima wanga zalefuka.+Mulungu ndiye thanthwe la mtima wanga ndiponso cholowa changa mpaka kalekale.+ Maliro 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ine ndanena kuti: “Yehova ndiye cholowa changa.+ Pa chifukwa chimenechi, ndidzakhala ndi mtima womudikira.”+
20 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Aroni, kuti: “Iwe udzakhala wopanda cholowa m’dziko mwawo, ndipo sudzapatsidwa gawo lililonse pakati pawo.+ Ine ndine gawo lako ndi cholowa chako pakati pa ana a Isiraeli.+
26 Thupi langa ndi mtima wanga zalefuka.+Mulungu ndiye thanthwe la mtima wanga ndiponso cholowa changa mpaka kalekale.+
24 Ine ndanena kuti: “Yehova ndiye cholowa changa.+ Pa chifukwa chimenechi, ndidzakhala ndi mtima womudikira.”+