Yesaya 26:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Usiku, mtima wanga umakulakalakani.+ Ndithu ndimakufunafunani ndi mtima wonse,+ chifukwa mukadzaweruza dziko lapansi,+ anthu okhala panthaka ya dzikolo adzaphunzira chilungamo.+ Chivumbulutso 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi ndani sadzakuopani,+ inu Yehova?+ Ndani sadzalemekeza dzina lanu?+ Pakuti inu nokha ndinu wokhulupirika.+ Mitundu yonse ya anthu idzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa malamulo anu olungama aonekera.”+
9 Usiku, mtima wanga umakulakalakani.+ Ndithu ndimakufunafunani ndi mtima wonse,+ chifukwa mukadzaweruza dziko lapansi,+ anthu okhala panthaka ya dzikolo adzaphunzira chilungamo.+
4 Kodi ndani sadzakuopani,+ inu Yehova?+ Ndani sadzalemekeza dzina lanu?+ Pakuti inu nokha ndinu wokhulupirika.+ Mitundu yonse ya anthu idzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa malamulo anu olungama aonekera.”+