Genesis 41:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Tsopano mufunefune munthu wozindikira ndi wanzeru, ndipo mumuike kukhala woyang’anira dziko la Iguputo.+ Genesis 41:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pamenepo Farao anafunsa antchito ake kuti: “Kodi pangapezekenso munthu wina wonga uyu, wokhala ndi mzimu wa Mulungu?”+ Yesaya 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Akalonga a ku Zowani+ ndi opusa ndithu. Malangizo a anthu anzeru ochokera pakati pa alangizi a Farao, ndi osathandiza.+ Kodi anthu inu mudzamuuza bwanji Farao kuti: “Ine ndine mwana wa anthu anzeru, mwana wa mafumu akale”?
33 “Tsopano mufunefune munthu wozindikira ndi wanzeru, ndipo mumuike kukhala woyang’anira dziko la Iguputo.+
38 Pamenepo Farao anafunsa antchito ake kuti: “Kodi pangapezekenso munthu wina wonga uyu, wokhala ndi mzimu wa Mulungu?”+
11 Akalonga a ku Zowani+ ndi opusa ndithu. Malangizo a anthu anzeru ochokera pakati pa alangizi a Farao, ndi osathandiza.+ Kodi anthu inu mudzamuuza bwanji Farao kuti: “Ine ndine mwana wa anthu anzeru, mwana wa mafumu akale”?