Salimo 78:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Pamapeto pake anapha ana onse oyamba kubadwa mu Iguputo,+Amene ndi chiyambi cha mphamvu zawo zobereka m’mahema a Hamu.+ Salimo 106:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Amene anachita zodabwitsa m’dziko la Hamu,+Amene anachita zochititsa mantha pa Nyanja Yofiira.+
51 Pamapeto pake anapha ana onse oyamba kubadwa mu Iguputo,+Amene ndi chiyambi cha mphamvu zawo zobereka m’mahema a Hamu.+