Ekisodo 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano, tamvera. Ndikutuma kwa Farao kuti ukatulutse anthu anga ana a Isiraeli ku Iguputo.”+ Ekisodo 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho pita. Ine ndidzakhala nawe polankhula ndipo ndidzakuuza zonena.”+ Ekisodo 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Pita kwa Farao, mfumu ya Iguputo,+ ukamuuze kuti alole ana a Isiraeli kutuluka m’dziko lake.”+ Salimo 77:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwatsogolera anthu anu ngati nkhosa,+Kudzera mwa Mose ndi Aroni.+ Machitidwe 7:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ine ndaona ndithu mmene anthu anga amene ali ku Iguputo akuwazunzira.+ Ndamva kubuula kwawo+ ndipo ndatsika kudzawalanditsa.+ Tsopano tamvera. Ndikufuna ndikutume ku Iguputo.’+
34 Ine ndaona ndithu mmene anthu anga amene ali ku Iguputo akuwazunzira.+ Ndamva kubuula kwawo+ ndipo ndatsika kudzawalanditsa.+ Tsopano tamvera. Ndikufuna ndikutume ku Iguputo.’+