32 Ndiyeno anthuwo anayamba kugwira zinzirizo. Anazigwira masana onse mpaka usiku wonse, mpakanso tsiku lotsatira osalekeza. Amene anagwira zokwana mahomeri 10+ ndiwo amene anagwira zochepa. Ndipo anali kuziyanika paliponse, moti zinangoti mbwee, pamsasa wonsewo.