Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 34:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mikango yamphamvu ingakhale ndi chakudya chochepa ndipo ingamve njala.+

      Koma ofunafuna Yehova sadzasowa chilichonse chabwino.+

  • Salimo 146:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Iye ndi Woperekera chiweruzo anthu ochitiridwa chinyengo,+

      Wopereka chakudya kwa anthu anjala.+

      Yehova amamasula anthu omangidwa.+

  • Yeremiya 31:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ansembe ndidzawatsitsimutsa ndi chakudya chochuluka,+ ndipo anthu anga ndidzawakhutiritsa ndi ubwino wanga,”+ watero Yehova.

  • Luka 1:53
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 53 Wakhutitsa anthu anjala ndi zinthu zabwino,+ amene anali ndi chuma wawapitikitsa chimanjamanja.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena