Salimo 57:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mtima wanga wakhazikika, Inu Mulungu,+Mtima wanga wakhazikika.Ndidzaimba nyimbo zokutamandani.+