Salimo 104:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndidzaimbira Yehova moyo wanga wonse.+Ndidzaimba nyimbo zotamanda Mulungu wanga nthawi yonse ya moyo wanga.+ Machitidwe 16:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma chapakati pa usiku,+ Paulo ndi Sila anali kupemphera ndi kutamanda Mulungu poimba nyimbo,+ ndipo akaidi ena anali kuwamva. Aefeso 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mukakhala pakati panu muziimba masalimo,+ nyimbo zotamanda+ Mulungu, ndiponso nyimbo zauzimu. Muziimba+ nyimbo zotamanda+ Yehova m’mitima mwanu,
33 Ndidzaimbira Yehova moyo wanga wonse.+Ndidzaimba nyimbo zotamanda Mulungu wanga nthawi yonse ya moyo wanga.+
25 Koma chapakati pa usiku,+ Paulo ndi Sila anali kupemphera ndi kutamanda Mulungu poimba nyimbo,+ ndipo akaidi ena anali kuwamva.
19 Mukakhala pakati panu muziimba masalimo,+ nyimbo zotamanda+ Mulungu, ndiponso nyimbo zauzimu. Muziimba+ nyimbo zotamanda+ Yehova m’mitima mwanu,