Salimo 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa nthawi ya zowawa zanga ndinaitana Yehova,Ndinafuulira Mulungu wanga kuti andithandize.+Iye anamva mawu anga ali m’kachisi wake.+Pamenepo makutu ake anamva kulira kwanga kopempha thandizo.+ Salimo 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova akuyankheni pa tsiku la nsautso.+Dzina la Mulungu wa Yakobo likutetezeni.+
6 Pa nthawi ya zowawa zanga ndinaitana Yehova,Ndinafuulira Mulungu wanga kuti andithandize.+Iye anamva mawu anga ali m’kachisi wake.+Pamenepo makutu ake anamva kulira kwanga kopempha thandizo.+